Marko 8:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo pomwepo analowa m'ngalawa ndi ophunzira ake, nafika ku mbali ya ku Dalamanuta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo pomwepo analowa m'ngalawa ndi ophunzira ake, nafika ku mbali ya ku Dalamanuta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pambuyo pake Yesu adatsazikana nawo anthu aja, kenaka Iye ndi ophunzira ake adaloŵa m'chombo napita ku dera la Dalamanuta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 analowa mʼbwato pamodzi ndi ophunzira ake napita ku dera la Dalamanuta. Onani mutuwo |