Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 8:4 - Buku Lopatulika

4 Ndipo ophunzira ake anamyankha Iye, kuti, Munthu adzatha kutenga kuti mikate yakukhutitsa anthu awa m'chipululu muno?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Ndipo ophunzira ake anamyankha Iye, kuti, Munthu adzatha kutenga kuti mikate yakukhutitsa anthu awa m'chipululu muno?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Ophunzira ake adamufunsa kuti, “Anthu ochuluka chotereŵa munthu angaŵapezere bwanji chakudya chokwanira, kuthengo ngati kuno?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ophunzira ake anayankha nati, “Kodi ndi kuti kuthengo kuno kumene munthu angapeze buledi okwanira kuwadyetsa?”

Onani mutuwo Koperani




Marko 8:4
10 Mawu Ofanana  

Pamenepo kazembe amene mfumu ankatsamira padzanja lake anamyankha munthu wa Mulungu, nati, Taonani, Yehova angachite mazenera m'mwamba chidzachitika ichi kodi? Nati iye, Taona, udzachiona ndi maso ako, koma iwe sudzadyako ai.


Ndipo ophunzira ananena kwa Iye, Tiione kuti mikate yotere m'chipululu yakukhutitsa unyinji wotere wa anthu?


pakuti sanazindikire za mikateyo, koma mitima yao inauma.


ndipo ngati ndiwauza iwo amuke kwao osadya kanthu, adzakomoka panjira; ndipo ena a iwo achokera kutali.


Ndipo anawafunsa, Muli nayo mikate ingati? Ndipo anati, Isanu ndi iwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa