Marko 8:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anawafunsa, Muli nayo mikate ingati? Ndipo anati, Isanu ndi iwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anawafunsa, Muli nayo mikate ingati? Ndipo anati, Isanu ndi iwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Yesu adaŵafunsa kuti, “Buledi ndiye muli naye mngati?” Iwo aja adati, “Msanu ndi muŵiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yesu anafunsa kuti, “Muli ndi malofu a buledi angati?” Iwo anayankha kuti, “Asanu ndi awiri.” Onani mutuwo |