Marko 8:3 - Buku Lopatulika3 ndipo ngati ndiwauza iwo amuke kwao osadya kanthu, adzakomoka panjira; ndipo ena a iwo achokera kutali. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo ngati ndiwauza iwo amuke kwao osadya kanthu, adzakomoka panjira; ndipo ena a iwo achokera kutali. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndikangoŵabweza kwao ali ndi njala chonchi, alefuka pa njira, chifukwa ena achokera kutali.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ngati nditawawuza kuti apite kwawo ali ndi njala, iwo adzakomoka mʼnjira chifukwa ena a iwo achokera kutali.” Onani mutuwo |