Marko 8:2 - Buku Lopatulika2 Ndimva nalo chifundo khamulo, chifukwa ali ndi Ine chikhalire masiku atatu, ndipo alibe kanthu kakudya: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndimva nalo chifundo khamulo, chifukwa ali ndi Ine chikhalire masiku atatu, ndipo alibe kanthu kakudya: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Ndikuŵamvera chifundo anthuŵa, chifukwa akhala nane masiku atatu tsopano, ndipo alibe chakudya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Ndili ndi chifundo ndi anthu awa; akhala ali ndi Ine masiku atatuwa ndipo alibe chakudya. Onani mutuwo |