Marko 8:1 - Buku Lopatulika1 Masiku ajawo pakukhalanso khamu lalikulu la anthu, ndipo analibe kanthu kakudya, Iye anadziitanira ophunzira ake, nanena nao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Masiku ajawo pakukhalanso khamu lalikulu la anthu, ndipo analibe kanthu kakudya, Iye anadziitanira ophunzira ake, nanena nao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pasanapite nthaŵi yaitali anthu ambirimbiri adasonkhananso. Pamene Yesu adaona kuti anthuwo alibe chakudya, adaitana ophunzira ake naŵauza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mʼmasiku amenewo gulu lina lalikulu la anthu linasonkhana. Popeza iwo analibe chakudya, Yesu anayitana ophunzira ake nati kwa iwo, Onani mutuwo |