Marko 8:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anadza ku Betsaida. Ndipo anadza naye kwa Iye munthu wakhungu, nampempha Iye kuti amkhudze. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anadza ku Betsaida. Ndipo anadza naye kwa Iye munthu wakhungu, nampempha Iye kuti amkhudze. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Yesu ndi ophunzira ake adafika ku Betsaida. Kumeneko anthu adabwera ndi munthu wakhungu, napempha Yesu kuti amchiritse pomkhudza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Iwo anafika ku Betisaida, ndipo anthu ena anabweretsa munthu wosaona ndipo anamupempha Yesu kuti amukhudze. Onani mutuwo |