Marko 8:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Iye ananena nao, Simudziwitsa ngakhale tsopano kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Iye ananena nao, Simudziwitsa ngakhale tsopano kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Apo Yesu adati, “Nanga ndiye simunamvetsebe?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Iye anawafunsa kuti, “Kodi simumvetsetsabe?” Onani mutuwo |