Marko 7:8 - Buku Lopatulika8 Musiya lamulo la Mulungu, nimusunga mwambo wa anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Musiya lamulo la Mulungu, nimusunga mwambo wa anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kenaka Yesu adati, “Inu mumasiya Malamulo a Mulungu, nkumasunga miyambo ya anthu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mwasiya malamulo a Mulungu ndipo mwagwiritsitsa miyambo ya anthu.” Onani mutuwo |