Marko 7:7 - Buku Lopatulika7 Koma andilambira Ine kwachabe, ndi kuphunzitsa maphunzitso, malangizo a anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Koma andilambira Iye kwachabe, ndi kuphunzitsa maphunzitso, malangizo a anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Amandipembedza inde, koma kupembedza kwaoko nkopanda phindu, chifukwa zimene amaphunzitsa ngati zophunzitsa zenizeni, ndi malamulo a anthu chabe.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Amandilambira Ine kwachabe; ndi kuphunzitsa malamulo ndi malangizo a anthu. Onani mutuwo |