Marko 7:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo ananena nao, Bwino mukaniza lamulo la Mulungu, kuti musunge mwambo wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo ananena nao, Bwino mukaniza lamulo la Mulungu, kuti musunge mwambo wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono popitiriza mau, Yesu adati, “Koma ndiye muli ndi njira yanu yochenjera yosiyira Malamulo a Mulungu kuti musunge miyambo yanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo anawawuzanso kuti, “Inu muli ndi njira yabwino yokankhira kumbali malamulo a Mulungu kuti mukatsatire miyambo yanuyo! Onani mutuwo |