Marko 7:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Afarisi ndi alembi anamfunsa Iye, kuti, Bwanji ophunzira anu satsata mwambo wa akulu, koma akudya mkate wao ndi m'manja mwakuda? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Afarisi ndi alembi anamfunsa Iye, kuti, Bwanji ophunzira anu satsata mwambo wa akulu, koma akudya mkate wao ndi m'manja mwakuda? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Choncho Afarisi ndi aphunzitsi a Malamulo aja adamufunsa Yesu kuti, “Chifukwa chiyani ophunzira anu sasunga mwambo wa makolo, koma amangodya chakudya osasamba m'manja moyenera?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Choncho Afarisi ndi aphunzitsi amalamulo anafunsa Yesu kuti, “Nʼchifukwa chiyani ophunzira anu satsatira mwambo wa makolo, mʼmalo mwake amangodya chakudya ndi mʼmanja mwakuda?” Onani mutuwo |