Marko 7:4 - Buku Lopatulika4 ndipo pakuchoka kumsika, sakudya osasamba m'thupi; ndipo zilipo zinthu zina zambiri anazilandira kuzisunga, ndizo matsukidwe a zikho, ndi miphika, ndi zotengera zamkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndipo pakuchoka kumsika, sakudya osasamba m'thupi; ndipo zilipo zinthu zina zambiri anazilandira kuzisunga, ndizo matsukidwe a zikho, ndi miphika, ndi zotengera zamkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndipo akachokera ku msika, saadya osasamba m'manja. Amasunganso miyambo ina yambiri imene makolo ao adaŵasiyira, monga kutsuka zikho, miphika, ndi ziŵiya zamkuŵa [ndi mabedinso.] Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Akabwera kuchokera ku msika samadya pokhapokha atasamba. Ndipo amasunga miyambo ina yambiri monga, kutsuka zikho, mitsuko ndi maketulo). Onani mutuwo |