Marko 7:3 - Buku Lopatulika3 Pakuti Afarisi, ndi Ayuda onse sakudya osasamba m'manja ao, kuti asungire mwambo wa akulu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuti Afarisi, ndi Ayuda onse sakudya osasamba m'manja ao, kuti asungire mwambo wa akulu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pajatu Afarisi ndi Ayuda ena onse saadya asanasambe m'manja mwa njira yoyenera. Amatero kuti asunge mwambo wa makolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 (Afarisi ndi Ayuda onse sadya pokhapokha atasamba mʼmanja, kusunga mwambo wa makolo awo. Onani mutuwo |