Marko 7:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo anachoka kunka kunyumba kwake, napeza mwana atamgoneka pakama, ndi chiwanda chitatuluka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo anachoka kunka kunyumba kwake, napeza mwana atamgoneka pakama, ndi chiwanda chitatuluka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Mai uja adabwerera kunyumba kwake, nakapezadi mwanayo ali gone pa bedi, mzimu woipa uja utatuluka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Atapita kwawo anakapeza mwana wake aligone pa bedi, chiwanda chitatuluka. Onani mutuwo |