Marko 7:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo anati kwa iye, Chifukwa cha mau amene, muka; chiwanda chatuluka m'mwana wako wamkazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo anati kwa iye, Chifukwa cha mau amene, muka; chiwanda chatuluka m'mwana wako wamkazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Apo Yesu adamuuza kuti, “Chifukwa cha mau mwanenaŵa, pitani, mzimu woipawo watuluka mwa mwana wanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ndipo Iye anamuwuza kuti, “Chifukwa cha yankholi, ukhoza kupita; chiwanda chachoka mwa mwana wako wamkazi.” Onani mutuwo |