Marko 7:22 - Buku Lopatulika22 zakuba, zakupha, zachigololo, masiriro, zoipa, chinyengo, chinyanso, diso loipa, mwano, kudzikuza, kupusa: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 zakuba, zakupha, zachigololo, masiriro, zoipa, chinyengo, chinyanso, diso loipa, mwano, kudzikuza, kupusa: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 zigololo, masiriro, kuipa mtima, kunyenga, zonyansa, kaduka, kunyoza, kudzikuza, ndiponso kupusa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 dyera, nkhwidzi, chinyengo, machitidwe onyansa, kaduka, chipongwe, kudzikuza ndi kupusa. Onani mutuwo |