Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 7:23 - Buku Lopatulika

23 zoipa izi zonse zituluka m'kati, nkudetsa munthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 zoipa izi zonse zituluka m'kati, nizidetsa munthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Zoipa zonsezi zimachokera m'kati mwa munthu, ndipo ndizo zimamuipitsa.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Zoyipa zonsezi zimatuluka mʼkati ndipo zimadetsa munthu.”

Onani mutuwo Koperani




Marko 7:23
8 Mawu Ofanana  

kulibe kanthu kunja kwa munthu kukalowa mwa iye, kangathe kumdetsa: koma zinthu zakutuluka mwa munthu, ndizo zakumdetsa munthu.


Ndipo ananena nao, Mutero inunso opanda nzeru kodi? Kodi simuzindikira kuti kanthu kalikonse kochokera kunja kukalowa mwa munthu, sikangathe kumdetsa iye;


Ndipo anati, Chotuluka mwa munthu ndicho chidetsa munthu.


zakuba, zakupha, zachigololo, masiriro, zoipa, chinyengo, chinyanso, diso loipa, mwano, kudzikuza, kupusa:


Ndipo Iye anauka nachoka kumeneko, nanka ku maiko a ku Tiro ndi Sidoni. Ndipo analowa m'nyumba, nafuna kuti asadziwe anthu; ndipo sanakhoze kubisika.


Ngati wina aononga Kachisi wa Mulungu, ameneyo Mulungu adzamuononga; pakuti Kachisi wa Mulungu ali wopatulika, ameneyo ndi inu.


Zonse ziyera kwa iwo amene ayera mtima; koma kwa iwo odetsedwa ndi osakhulupirira kulibe kanthu koyera; komatu zadetsedwa nzeru zao ndi chikumbumtima chao.


Momwemonso iwo m'kulota kwao adetsa matupi ao, napeputsa ufumu, nachitira mwano maulemerero.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa