Marko 7:21 - Buku Lopatulika21 Pakuti m'kati mwake mwa mitima ya anthu, mutuluka maganizo oipa, zachiwerewere, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pakuti m'kati mwake mwa mitima ya anthu, mutuluka maganizo oipa, zachiwerewere, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Chifukwa m'kati mwa mitima ya anthu ndiye mumatuluka maganizo oipa, za chiwerewere, za kuba, za kuphana, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pakuti kuchokera mʼkati mwa mitima ya anthu, mumatuluka maganizo oyipa, chiwerewere, kuba, kupha, chigololo, Onani mutuwo |