Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 7:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo anasonkhana kwa Iye Afarisi, ndi alembi ena, akuchokera ku Yerusalemu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo anasonkhana kwa Iye Afarisi, ndi alembi ena, akuchokera ku Yerusalemu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Tsiku lina Afarisi ena pamodzi ndi aphunzitsi ena a Malamulo, amene adaachokera ku Yerusalemu, adasonkhana kwa Yesu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Afarisi ndi ena mwa aphunzitsi amalamulo omwe anachokera ku Yerusalemu anasonkhana momuzungulira Yesu ndipo

Onani mutuwo Koperani




Marko 7:1
5 Mawu Ofanana  

Ndipo alembi amene adatsika ku Yerusalemu ananena kuti, Ali naye Belezebulu, ndipo, Ndi mkulu wao wa ziwanda atulutsa ziwanda.


ndipo anaona kuti ophunzira ake ena anadya mkate ndi m'manja mwakuda, ndiwo osasamba.


Ndipo panali tsiku limodzi la masiku awo, Iye analikuphunzitsa; ndipo analikukhalapo Afarisi ndi aphunzitsi a malamulo, amene anachokera kumidzi yonse ya ku Galileya, ndi Yudeya ndi Yerusalemu: ndipo mphamvu ya Ambuye inali ndi Iye yakuwachiritsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa