Marko 6:8 - Buku Lopatulika8 ndipo anawauza kuti asatenge kanthu ka paulendo, koma ndodo yokha; asatenge mkate, kapena thumba, kapena ndalama m'lamba lao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ndipo anawauza kuti asatenge kanthu ka paulendo, koma ndodo yokha; asatenge mkate, kapena thumba, kapena ndalama m'lamba lao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Adaŵalamula kuti, “Musatenge kanthu kena kalikonse pa ulendo, koma ndodo yokha. Musatenge kamba, kapena thumba lapaulendo, kapena ndalama m'chikwama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Zomwe anawalangiza ndi izi: “Musatenge kanthu ka paulendo koma ndodo yokha; osatenga buledi, thumba, kapena ndalama. Onani mutuwo |