Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 6:53 - Buku Lopatulika

53 Ndipo ataoloka iwo, anafika pamtunda ku Genesarete, nakocheza padooko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

53 Ndipo ataoloka iwo, anafika pamtunda ku Genesarete, nakocheza padooko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

53 Yesu ndi ophunzira ake adaoloka nyanja, nakafika ku Genesarete, nkuimitsa chombo kumeneko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

53 Atawoloka, anafika ku Genesareti nayima pa dooko.

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:53
4 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene anatuluka m'ngalawa anamzindikira pomwepo,


Ndipo panali, pakumkanikiza khamu la anthu, kudzamva mau a Mulungu, Iye analikuimirira m'mbali mwa nyanja ya Genesarete;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa