Marko 6:54 - Buku Lopatulika54 Ndipo pamene anatuluka m'ngalawa anamzindikira pomwepo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201454 Ndipo pamene anatuluka m'ngalawa anamzindikira pomwepo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa54 Pamene iwo adatuluka m'chombomo, nthaŵi yomweyo anthu adamzindikira Yesu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero54 Atangotuluka mʼbwato, anthu anamuzindikira Yesu. Onani mutuwo |