Marko 6:16 - Buku Lopatulika16 Koma Herode pamene anamva, ananena, Yohane amene ndamdula mutu, wauka iyeyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma Herode pamene anamva, ananena, Yohane amene ndamdula mutu, wauka iyeyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pamene Herode adamva zimenezi, adati, “Yohane yemwe ndidamdula pakhosi uja ndiye adauka kwa akufayu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma Herode atamva zimenezi anati, “Yohane, munthu amene ndinamudula mutu, waukitsidwa kuchokera kwa akufa.” Onani mutuwo |