Marko 6:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Iye anatuluka kumeneko; nafika kudziko la kwao; ndipo ophunzira ake anamtsata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Iye anatuluka kumeneko; nafika kudziko la kwao; ndipo ophunzira ake anamtsata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Yesu adachoka kumeneko, nakafika kumudzi kwao. Ophunzira ake adatsagana naye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yesu anachoka kumeneko napita ku mudzi kwawo, pamodzi ndi ophunzira ake. Onani mutuwo |