Marko 5:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo anawalamulira kwambiri kuti asadziwe ichi munthu mmodzi, nawauza kuti ampatse iye kudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo anawalamulira kwambiri kuti asadziwe ichi munthu mmodzi, nawauza kuti ampatse iye kudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Koma Yesu adaŵalamula mwamphamvu kuti zimenezo wina aliyense asazidziŵe. Kenaka adaŵauza kuti ampatse chakudya mtsikanayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Anawalamulira kwambiri kuti asawuze wina aliyense za ichi, ndipo anawawuza kuti amupatse kanthu koti adye. Onani mutuwo |