Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 5:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo anamfunsa, Dzina lako ndani? Ndipo ananena kwa Iye, Dzina langa ndine Legio; chifukwa tili ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo anamfunsa, Dzina lako ndani? Ndipo ananena kwa Iye, Dzina langa ndine Legio; chifukwa tili ambiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Tsono Yesu adamufunsa munthuyo kuti, “Dzina lako ndani?” Iye adayankha kuti, “Dzina langa ndine ‘Chigulu,’ chifukwa tilipo ochuluka.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ndipo Yesu anamufunsa iye, “Dzina lako ndani?” Iye anayankha kuti, “Dzina langa ndine Legiyo, pakuti tilipo ambiri.”

Onani mutuwo Koperani




Marko 5:9
7 Mawu Ofanana  

Pomwepo upita, nutenga pamodzi ndi uwu mizimu ina inzake isanu ndi iwiri yoipa yoposa mwini yekhayo, ndipo ilowa, nikhalamo. Ndipo matsirizidwe ake a munthu uyo akhala oipa oposa mayambidwe ake. Kotero kudzakhalanso kwa obadwa oipa amakono.


Kapena uganiza kuti sindingathe kupemphera Atate wanga, ndipo Iye adzanditumizira tsopano lino mabungwe a angelo oposa khumi ndi awiri?


Ndipo anampempha Iye kwambiri kuti asaitulutsire kunja kwake kwa dziko.


Ndipo anadza kwa Yesu, napenya wogwidwa ziwandayo alikukhala pansi, wovala ndi wa nzeru zake zabwino, ndiye amene anali ndi legio; ndipo anaopa iwo.


Pakuti ananena kwa iye, Tuluka iwe, mzimu wonyansa, kwa munthuyu.


Ndipo Yesu anamfunsa iye, kuti, Dzina lako ndiwe yani? Ndipo anati, Legio, chifukwa ziwanda zambiri zidalowa mwa iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa