Marko 5:8 - Buku Lopatulika8 Pakuti ananena kwa iye, Tuluka iwe, mzimu wonyansa, kwa munthuyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pakuti ananena kwa iye, Tuluka iwe, mzimu wonyansa, kwa munthuyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Adaatero chifukwa Yesu anali atanena kuti, “Mzimu woipawe, tuluka mwa munthuyu!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pakuti Yesu anati kwa iye, “Tuluka mwa munthuyu, iwe mzimu woyipa!” Onani mutuwo |