Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 5:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo anampempha Iye kwambiri kuti asaitulutsire kunja kwake kwa dziko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo anampempha Iye kwambiri kuti asaitulutsire kunja kwake kwa dziko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ndipo iye adadandaulira Yesu kwambiri kuti mizimuyo asaitulutsire kunja kwa dera limenelo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ndipo anamupempha Yesu mobwerezabwereza kuti asazitulutse mʼderalo.

Onani mutuwo Koperani




Marko 5:10
4 Mawu Ofanana  

Ndipo alembi amene adatsika ku Yerusalemu ananena kuti, Ali naye Belezebulu, ndipo, Ndi mkulu wao wa ziwanda atulutsa ziwanda.


Ndipo panali pamenepo gulu lalikulu la nkhumba zilinkudya kuphiri.


Ndipo anailola. Ndipo mizimu yonyansa inatuluka, nilowa mu nkhumba; ndipo gulu linatsika liwiro potsetsereka ndi kulowa m'nyanja, ndizo ngati zikwi ziwiri; ndipo zinatsamwa m'nyanja.


Ndipo anamfunsa, Dzina lako ndani? Ndipo ananena kwa Iye, Dzina langa ndine Legio; chifukwa tili ambiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa