Marko 5:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo panali pamenepo gulu lalikulu la nkhumba zilinkudya kuphiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo panali pamenepo gulu lalikulu la nkhumba zilinkudya kuphiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pafupi pomwepo, pachitunda poteropo, pankadya gulu lalikulu la nkhumba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Gulu lalikulu la nkhumba limadya mʼmbali mwa phiri limene linali pafupi. Onani mutuwo |