Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 5:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo masiku onse, usiku ndi usana, anakhala m'manda ndi m'mapiri, nafuula, nadzitematema ndi miyala.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo masiku onse, usiku ndi usana, anakhala m'manda ndi m'mapiri, nafuula, nadzitematema ndi miyala.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Usana ndi usiku ankakhala kumandako ndi m'mapiri, akumangofuula ndi kudzipweteka ndi miyala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Usana ndi usiku ankakhala ku manda ndi kumapiri, akulira ndi kudzicheka ndi miyala.

Onani mutuwo Koperani




Marko 5:5
5 Mawu Ofanana  

Ndipo anakwezadi mau, nadzitema monga makhalidwe ao ndi mipeni ndi nthungo, kuti mwazi wao unali chuchuchu.


pakuti ankamangidwa kawirikawiri ndi matangadza ndi maunyolo, ndipo anamwetula maunyolo, naduladula matangadza; ndipo palibe munthu anali ndi mphamvu yakumfuya.


Ndipo pakuona Yesu kutali, anathamanga, namgwadira Iye;


Inu muli ochokera mwa atate wanu mdierekezi, ndipo zolakalaka zake za atate wanu mufuna kuchita. Iyeyu anali wambanda kuyambira pachiyambi, ndipo sanaime m'choonadi, pakuti mwa iye mulibe choonadi. Pamene alankhula bodza, alankhula za mwini wake; pakuti ali wabodza, ndi atate wake wa bodza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa