Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 5:26 - Buku Lopatulika

26 ndipo anamva zowawa zambiri ndi asing'anga ambiri, nalipira zonse anali nazo osachira pang'ono ponse, koma makamaka nthenda yake idakula,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 ndipo anamva zowawa zambiri ndi asing'anga ambiri, nalipira zonse anali nazo osachira pang'ono ponse, koma makamaka nthenda yake idakula,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Adaazunzika zedi ndi asing'anga ochuluka amene ankayesa kumuchiza. Mwakuti adaamwaza chuma chake chonse, komabe osapeza bwino konse. M'malo mwake matendawo analikunka nakulirakulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Iye anavutika kwambiri pamene asingʼanga ambiri ankamusamalira ndipo anagwiritsa ntchito zonse anali nazo, koma mʼmalo mochira, nthenda yake inkakulakulabe.

Onani mutuwo Koperani




Marko 5:26
8 Mawu Ofanana  

Koma inu ndinu opanga zabodza, asing'anga opanda pake inu nonse.


Tithandizeni mumsauko; pakuti chipulumutso cha munthu ndi chabe.


Babiloni wagwa dzidzidzi naonongedwa; mumkuwire iye; mutengere zowawa zake vunguti, kapena angachire.


Kodi mulibe vunguti mu Giliyadi? Kodi mulibe sing'anga m'menemo; analekeranji kuchira mwana wamkazi wa anthu anga?


Ndipo munthu wamkazi amene anali ndi nthenda yachidwalire zaka khumi ndi ziwiri,


m'mene iye anamva mbiri yake ya Yesu, anadza m'khamu kumbuyo kwake, nakhudza chovala chake.


Ndipo mkazi, anali ndi nthenda yachidwalire zaka khumi ndi ziwiri, amene adasudzula asing'anga za moyo wake zonse, ndipo sanathe kuchiritsidwa ndi mmodzi yense,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa