Marko 5:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo munthu wamkazi amene anali ndi nthenda yachidwalire zaka khumi ndi ziwiri, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo munthu wamkazi amene anali ndi nthenda yachidwalire zaka khumi ndi ziwiri, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono panali mai wina amene adakhala akuvutika ndi matenda a msambo pa zaka khumi ndi ziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pomwepo panali mayi amene amadwala nthenda yotaya magazi kwa zaka khumi ndi ziwiri. Onani mutuwo |