Marko 5:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo anafika tsidya lina la nyanja, kudziko la Agerasa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo anafika tsidya lina la nyanja, kudziko la Agerasa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Tsono Yesu ndi ophunzira ake adafika ku tsidya la Nyanja ya Galileya, ku dera la Agerasa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndipo anawoloka nyanja napita ku dera la Gerasa. Onani mutuwo |