Marko 5:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo pamene adatuluka mungalawa, pomwepo anakomana naye munthu wotuluka kumanda wa mzimu wonyansa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo pamene adatuluka mungalawa, pomwepo anakomana naye munthu wotuluka kumanda wa mzimu wonyansa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Yesu atangotuluka m'chombo, munthu wina wogwidwa ndi mzimu woipa adadzakumana naye kuchokera ku manda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Yesu atatuluka mʼbwato, munthu amene anali ndi mzimu woyipa anachoka ku manda ndi kukumana naye. Onani mutuwo |