Marko 4:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo ananena, Tidzafaniziranji Ufumu wa Mulungu? Kapena tidzaulinganiza ndi fanizo lotani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo ananena, Tidzafaniziranji Ufumu wa Mulungu? Kapena tidzaulinganiza ndi fanizo lotani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Yesu adatinso, “Kodi Ufumu wa Mulungu tingauyerekeze ndi chiyani? Kaya tiwufanizire ndi chiyani? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndipo anatinso, “Kodi tinene kuti ufumu wa Mulungu ufanana ndi chiyani, kapena ndi fanizo lotani limene tidzagwiritsa ntchito pakuwufotokozera? Onani mutuwo |