Marko 4:29 - Buku Lopatulika29 Pakucha zipatso, pamenepo atenga chisenga, pakuti nthawi yakumweta yafika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Pakutcha zipatso, pamenepo atenga chisenga, pakuti nthawi yakumweta yafika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Tsono mbeuzo zikacha, munthu uja amatenga mpeni wodulira, pakuti nyengo yokolola yafika.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Mbewuyo ikangokhwima, amayimweta chifukwa nthawi yokolola yakwana.” Onani mutuwo |