Marko 4:3 - Buku Lopatulika3 Mverani: taonani, wofesa anatuluka kukafesa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mverani: taonani, wofesa anatuluka kukafesa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 “Mvetsetsani! Munthu wina adapita kukafesa mbeu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 “Tamverani! Mlimi anapita kukafesa mbewu zake. Onani mutuwo |