Marko 4:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo anawaphunzitsa zinthu zambiri m'mafanizo, nanena nao m'chiphunzitso chake, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo anawaphunzitsa zinthu zambiri m'mafanizo, nanena nao m'chiphunzitso chake, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 ndipo Yesu adayamba kuŵaphunzitsa zambiri m'mafanizo. Poŵaphunzitsa adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Anawaphunzitsa zinthu zambiri mʼmafanizo, ndipo mʼchiphunzitso chake anati: Onani mutuwo |