Marko 4:25 - Buku Lopatulika25 Pakuti kwa iye amene ali nako kanthu, kadzapatsidwa; ndipo kwa iye amene alibe kanthu, kadzachotsedwa ngakhale kanthu kalikonse ali nako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pakuti kwa iye amene ali nako kanthu, kadzapatsidwa; ndipo kwa iye amene alibe kanthu, kadzachotsedwa ngakhale kanthu kalikonse ali nako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Paja amene ali ndi kanthu kale, adzamuwonjezera zina. Koma amene alibe kanthu, ngakhale kamene ali nakoko adzamlandabe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka; amene alibe, ngakhale zimene ali nazo zidzachotsedwa kwa iwo.” Onani mutuwo |