Marko 4:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo ananena ndi iwo, Kodi atenga nyali kuti akaivundikire mbiya, kapena akaiike pansi pa kama, osati kuti akaiike pa choikapo chake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo ananena ndi iwo, Kodi atenga nyali kuti akaivundikire mbiya, kapena akaiike pansi pa kama, osati kuti akaiike pa choikapo chake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono Yesu adaŵafunsa kuti, “Kodi anthu amatenga nyale nkuivundikira ndi mbiya, kapena kuibisa kunsi kwa bedi? Suja amaiika pa malo oonekera? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Iye anawawuza kuti, “Kodi umatenga nyale ndi kuyiika pansi pa mbiya kapena pansi pa bedi? Mʼmalo mwake, kodi simuyika pa choyikapo chake? Onani mutuwo |