Marko 4:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo ananena nao, Simudziwa kodi fanizo ili? Mukazindikira bwanji mafanizo onse? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo ananena nao, Simudziwa kodi fanizo ili? Mukazindikira bwanji mafanizo onse? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Pambuyo pake Yesu adaŵafunsa kuti, “Monga simukulimvetsadi fanizo limeneli? Nanga mudzamvetsa bwanji fanizo lina lililonse? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Pamenepo Yesu anawawuza kuti, “Kodi simukulimvetsa fanizoli? Kodi nanga mudzazindikira bwanji fanizo lina lililonse? Onani mutuwo |