Marko 3:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo nyumba ikagawanika pa iyo yokha, singathe kukhazikika nyumbayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo nyumba ikagawanika pa iyo yokha, sikhoza kukhazikika nyumbayo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ndipo anthu a m'banja limodzi akayamba kugaŵikana, banja lotere silingalimbe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ngati nyumba igawanikana mwa iyo yokha, nyumba imeneyo singathe kuyima. Onani mutuwo |