Marko 3:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo Satana akadziukira mwini yekha, nagawanika, sangathe kukhazikika, koma atsirizika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo Satana akadziukira mwini yekha, nagawanika, sakhoza kukhazikika, koma atsirizika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Tsono ngati a mu ufumu wa Satana aukirana okhaokha nagaŵikana, Satanayo sangalimbe, ndiye kuti watha basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ndipo ngati Satana adzitsutsa yekha sangathe kuyima; ulamuliro wake watha. Onani mutuwo |