Marko 3:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo ufumu ukagawanika pa uwu wokha, sungathe kukhazikika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo ufumu ukagawanika pa uwu wokha, sukhoza kukhazikika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Anthu a mu ufumu uliwonse akayamba kuukirana, ufumuwo sungalimbe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Ngati ufumu ugawanikana mwa iwo okha, ufumu umenewo sungakhalitse. Onani mutuwo |