Marko 3:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo m'mene adawaitana iwo, ananena nao m'mafanizo, Satana angathe bwanji kutulutsa Satana? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo m'mene adawaitana iwo, ananena nao m'mafanizo, Satana angathe bwanji kutulutsa Satana? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Tsono Yesu adaitana anthu kuti adze pafupi, nanena mwafanizo kuti, “Kodi a mu ufumu wa Satana angathe bwanji kutulutsana okhaokha? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Pamenepo Yesu anawayitana nawayankhula mʼmafanizo nati: “Kodi Satana angatulutse bwanji Satana? Onani mutuwo |