Marko 3:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anaika khumi ndi awiri, kuti akhale ndi Iye, ndi kuti akawatume kulalikira, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anaika khumi ndi awiri, kuti akhale ndi Iye, ndi kuti akawatume kulalikira, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono adasankhapo khumi ndi aŵiri, naŵatcha dzina loti, “Atumwi.” Adaŵauza kuti, “Ndasankha inu kuti muzikhala nane, ndidzakutumani kukalalika, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Iye anasankha khumi ndi awiri, nawayika akhale atumwi; pokhala ndi Iye aziwatuma kukalalikira Onani mutuwo |