Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 3:13 - Buku Lopatulika

13 Ndipo anakwera m'phiri, nadziitanira iwo amene anawafuna Iye mwini; ndipo anadza kwa Iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Ndipo anakwera m'phiri, nadziitanira iwo amene anawafuna Iye mwini; ndipo anadza kwa Iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Yesu adakwera ku phiri, ndipo adaitana anthu amene Iye mwini ankaŵafuna, iwo nkupitadi kumene kunali Iyeko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Yesu anakwera ku phiri ndipo anayitana amene anawafuna, ndipo anabwera kwa Iye.

Onani mutuwo Koperani




Marko 3:13
7 Mawu Ofanana  

Ndipo m'mene Iye anaona makamu, anakwera m'phiri; ndipo m'mene Iye anakhala pansi, anadza kwa Iye ophunzira ake;


Ndipo anaika khumi ndi awiri, kuti akhale ndi Iye, ndi kuti akawatume kulalikira,


Ndipo anadziitanira khumi ndi awiriwo, nayamba kuwatumiza iwo awiriawiri; nawapatsa mphamvu pa mizimu yonyansa;


Ndipo Iye anaitana pamodzi khumi ndi awiriwo nawapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse, ndi zakuchiritsa nthenda.


Koma Yesu anakwera kuphiri, nakhala pansi komweko pamodzi ndi ophunzira ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa