Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Marko 3:15 - Buku Lopatulika

15 ndi kuti akhale nao ulamuliro wakutulutsa ziwanda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 ndi kuti akhale nao ulamuliro wakutulutsa ziwanda.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 ndipo mudzakhala ndi mphamvu zotulutsira mizimu yoipa.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 ndi kuti akhale ndi ulamuliro wotulutsa ziwanda.

Onani mutuwo Koperani




Marko 3:15
3 Mawu Ofanana  

Ndipo mbiri yake inabuka ku Siriya konse: ndipo anatengera kwa Iye onse akudwala, ogwidwa ndi nthenda ndi mazunzo a mitundumitundu, ndi ogwidwa ndi ziwanda, ndi akhunyu, ndi amanjenje; ndipo Iye anawachiritsa.


Ndipo anaika khumi ndi awiri, kuti akhale ndi Iye, ndi kuti akawatume kulalikira,


Ndipo Simoni anamutcha Petro;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa