Marko 3:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo mizimu yonyansa, m'mene inamuona Iye, inamgwadira, nifuula, niti, Inu ndinu Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo mizimu yonyansa, m'mene inamuona Iye, inamgwadira, nifuula, niti, Inu ndinu Mwana wa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mizimu yoipa inkati ikamuwona, inkadzigwetsa pansi pafupi ndi Iye nkumafuula kuti, “Inu ndinu Mwana wa Mulungu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Nthawi iliyonse mizimu yoyipa ikamuona, imagwa pansi pamaso pake ndi kufuwula kuti, “Inu ndinu Mwana wa Mulungu!” Onani mutuwo |